Ngati Mumakonda Ambuye
Kodi mumakonda Ambuye? Limeli ndi funso lofunika kwambiri! Ambuye athu, Yesu Khristu, anafunsa Petro kuti, "Petro, umandikonda?" N'chifukwa chiyani chikondi chanu pa Mulungu chiri chinthu chimene tiyenera kukambirana? Yesu akunena kuti lamulo lalikulu kwambiri ndi lakuti: "Uzikonda Ambuye Mulungu wako, ndi mtima wako wonse, ndi moyo wako wonse, ndi nzeru zako zonse." Nthawi zina, pamakhala zochitika zimene Ambuye amalola kuti zibwere pamoyo panu—zochitika zimene zimangokhala mayeso, mayeso otsimikizira chikondi chanu kwa Ambuye. Ngati mumakonda Ambuye, tsimikizani chikondi chanu mwa kupambana mayeso a chikondi! Buku lina lodabwitsa lolembedwa ndi wolemba wodziwika bwino, Dag Heward-Mills, lidzakupangitsani kuganiza mozama ndi kudzifunsa funso lofunika koposa: "Kodi ndimamukonda Ambuye kwenikweni?"
-
Autore:
-
Anno edizione:2025
-
Editore:
-
Formato:
-
Lingua:Inglese
Formato:
Gli eBook venduti da Feltrinelli.it sono in formato ePub e possono essere protetti da Adobe DRM. In caso di download di un file protetto da DRM si otterrà un file in formato .acs, (Adobe Content Server Message), che dovrà essere aperto tramite Adobe Digital Editions e autorizzato tramite un account Adobe, prima di poter essere letto su pc o trasferito su dispositivi compatibili.
Cloud:
Gli eBook venduti da Feltrinelli.it sono sincronizzati automaticamente su tutti i client di lettura Kobo successivamente all’acquisto. Grazie al Cloud Kobo i progressi di lettura, le note, le evidenziazioni vengono salvati e sincronizzati automaticamente su tutti i dispositivi e le APP di lettura Kobo utilizzati per la lettura.
Clicca qui per sapere come scaricare gli ebook utilizzando un pc con sistema operativo Windows